Zwii♥️ Profile Banner
Zwii♥️ Profile
Zwii♥️

@Tawonga70129690

Followers
4,606
Following
5,069
Media
25
Statuses
5,434

komabe njoya🔥

Malawi🇲🇼
Joined July 2019
Don't wanna be here? Send us removal request.
Explore trending content on Musk Viewer
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Ineyo I was about to celebrate my 100 followers winanso mkuzandipanga unfollow,mkupezeka ndili pa 99😭😭 Ndalakwa chani anganya😂😂😂😂😂
58
23
340
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Chuma chili mu nthaka😉
Tweet media one
21
19
281
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 month
My brother used to show flames my father with his bad behavior back in the days,now he is getting double from his son..apa mpamene ndadziwa kuti magwafa sabereka masuku😂😂
18
52
279
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
@GwambaOfficial Popita kumeneko mwayenda wapansi??
41
33
271
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 months
Pa ukwatipo akazafuna microphone muzamukanize ndi mbama yakukamwa🤭
22
54
256
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Hie,my name is so so so..I've sent you a direct message because I want us to be friends or whatever....izizi zimavuta pati boyizi??😂mmadziwa kuti hie yekha amavuta kuyankha??hie kumangosanjikizana?
98
34
235
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
After yesterdays convo with @CEO_Ngozo I decided to try out advertising my make up business...Magaye ndimaphoda ndithu..this is a phone camera pic,no edit,no filter... support my business am in Blantyre soche..you can reach me anyday and anytime...0993033562.
Tweet media one
9
60
182
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Umakhala ungoziyendera zawekha..wina amangobwera amvekere "sungavutike mkugula mattress munthu"..like tf??😂😂
@wangi_blessed
🌼A_Fine_Marshmallow 🍃
1 year
Koma ma duntu tikati tinyozeke Pena eh🙌😂😂
23
14
81
34
34
183
@Tawonga70129690
Zwii♥️
9 months
2023 was great.. looking forward to 2024..the machine behind me is not mine..mungazati I live a fake life titakumana mu za kwale🤭
Tweet media one
@Cisp441
B O B B Y
9 months
Since 2023 is coming to an end Quote this tweet with your favourite picture of 2023
Tweet media one
56
17
283
27
13
183
@Tawonga70129690
Zwii♥️
4 months
I may act like I'm okay,but deep down in my heart ka caption kaja kokuti "ife nde tikuthawenitu" with your passport in your hands kamandipweteka😌
8
52
183
@Tawonga70129690
Zwii♥️
3 months
Sukavutika kugula mattress aise!!😂
@FaijoProsper
FAIJO PROSPER 🇲🇼
3 months
Anati chani anthuwa atakuonani mukuyenda ndi chibwenzi chanu
Tweet media one
65
28
228
14
14
171
@Tawonga70129690
Zwii♥️
9 months
Are we allowed to participate alimife?🤔
Tweet media one
12
7
162
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Call me Old school but immediately someone texts me in "hud" or "wud" am no longer interested in that macheza..fenks😂
19
34
155
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Yes maiwo ndiopanda nzeru...but dragging zeze's father in this useless narratives is senseless...being ineyo mwana wa a driver izizi zandikwiitsa kobasi.
@yamikani_moloko
Accused Number One 🇲🇼
1 year
Akuterotu kuseliku....
Tweet media one
31
21
78
22
11
156
@Tawonga70129690
Zwii♥️
7 months
Mnanena ine...okudya sudzampeza akupanga comment😂..amakhala Ali phee game kumangoionera patali.
11
32
157
@Tawonga70129690
Zwii♥️
3 months
Koma mwati Blantyre amene ndimakhala ineyo ndi uti??I don't even know a single soul mentioned there😂..ayi zikomo
29
15
160
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Waking up to my birthday!!God's Grace is always sufficient 😍 Lero birthday ya Zwitso kwachema☺️
Tweet media one
22
8
147
@Tawonga70129690
Zwii♥️
8 months
After bringing screenshots here then what??come on...
30
50
143
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
@zodiakonline Zimayenda mchinsisitu eti...mukakayamba kuvutika kumeneko ziziyendenso mchisisi..osati kumabwera mkumati amalawi tithandizeni mutisonkhele ndalama tizibwerako kuno aluya akumatizunza.
11
29
143
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
🥱
Tweet media one
14
29
143
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Kunja kuno kukuchitika zinthu zoophya🤔 Magaye tiyeni tizipemphela!
4
34
130
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
How do y'all manage Instagram??eh eh.. bundle kumangouluka??😏ayi ndalephera ndineyo fenks
24
18
125
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 months
Eheh..ine Ndimati changati ine chapolama apachi nde chitinso ichi😂
@DavidMpha
Gufe
2 months
Zokongoletsa sofa motere m'makomomu zilipobe?
Tweet media one
38
8
98
32
11
126
@Tawonga70129690
Zwii♥️
4 months
One this I would never understand is how some men try to form gangster in church by not clapping hands or singing songs together with the church...ndeno mmadzatani ku church?🤔
14
17
120
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 months
I once blocked someone on Whatsapp and left his Facebook account unblocked,,mnangoona chi message kuti koma pamene titazakumane iwe ndi ine nde ndizakuponda😂😂..ine nde ndiphulitsidwa basi!!!
18
10
110
@Tawonga70129690
Zwii♥️
9 months
Kodi ndekuti azibambo,creating funny content osavala zovala zachibebi sizimatheka??🤔
22
16
105
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
Ine nde am not against Walter because I don't follow football that much for me to know zimene amasokoneza kumeneko,,the only reason I want mr Haiya to win is because he was once a fundraising chair ku church kwathu and things were much smooth and organised 😂..mbwenu!!
14
17
102
@Tawonga70129690
Zwii♥️
14 days
Bola kumamwa izi..sizimapatsa matsire😊
Tweet media one
15
7
102
@Tawonga70129690
Zwii♥️
3 months
Tweet media one
@kaonde_king
Ronald ///
3 months
Your favourite photo/video from the first half of the year.🤲🏿
21
18
86
10
6
101
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
The last time I did,I was rejected 😂😂sinzayelekezanso..ndi ntchito ya amuna iyi
@CrazyGuy_MW
m.m.
1 year
Do women actually approach men first or Enafe mdi onyasa 😭😂😂
8
7
30
33
18
95
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 days
Tweet media one
5
12
88
@Tawonga70129690
Zwii♥️
4 months
Jeremiah 29vs11
Tweet media one
@uncle_stunt
MR CHAFUWA JNR🇲🇼🇿🇦📽️📹
4 months
Picture with your favorite verse Isaiah 60 vs 22
Tweet media one
10
16
71
4
14
86
@Tawonga70129690
Zwii♥️
9 months
Kulimbikira nde tikulimbikira..koma vuto ndi anzathu omwewa okanika kubwenza ngongole zathuwa..Afiti!!
7
30
83
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 month
Whatever is happening I'm sure I will still get the gist..wina apezeka aing'alura ndithu.
4
14
84
@Tawonga70129690
Zwii♥️
11 months
Apa pokha ndiseke Kaye😂
@aubette_
That Lilongwe Guy 🇲🇼🏀
11 months
Ndithudi🤌🏾
Tweet media one
14
42
202
4
8
79
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Then there is us.. whether it's weekend or weekdays,we don't see the difference 😂kungokhala bwenzi la pakhomo basi!! Kutsala pang'ono kusanduka furniture!
9
12
77
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
How can one treat "kuiwala pafupipafupi"...it's getting worse iih
35
10
74
@Tawonga70129690
Zwii♥️
8 months
Ikakhala Bet nde ndungodyedwa...ndizisiyatu ine zimenezi!
19
13
70
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Chuma kumadya ndi abale Anu magaye!!!don't be in a hurry kukondweretsa anzako pamene m'bale wako sanakondwere✌️
5
11
71
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Komanso ineyo sindingasiye kubeta magaye😂😂😂 One day is one day ndizadya million
8
8
68
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
For a moment,I thought it was Malawian kwacha...got carried away🤭
@AbrahamMacHILLS
Engr. Rev. Abraham MacHILLS, (Ph.D)
1 year
With 5M, I can build this 2 bedroom house for you, if you already have a land.
Tweet media one
10K
15K
71K
13
1
68
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Tweet media one
@refilwepoetry93
Refilwe Ntopa
1 year
Quote or comment with a picture of you Happy and don’t forget to #Kusangalala Because @Zeze_Kingston deserves his flowers 🙌🏽💐
Tweet media one
78
94
581
4
7
66
@Tawonga70129690
Zwii♥️
20 days
Ati Inu amenewo a "Zwii"..hehe lodyera limenelo??😂😂my husband can be dramatic sometimes,I realized it was the first time coming across my twitter account 😂
6
7
63
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Someone once told me that "ndalama zimapita ku ndalama zinzake"..how true is this?🤔
16
8
61
@Tawonga70129690
Zwii♥️
11 months
It doesn't hurt kukhala bwino ndi anthu magaye,,a certain friend has been checking on me on a daily basis chigwereni kumowa🤭..mind you this friend is from way back,,I worked with him in 2014.. sometimes I kinda lose his contact but he never gets rid of mine 😀..ndine waphindu😂
20
4
58
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Basi blesser wakupatsani 30 thousand,Inu kukamwa mweee...aaah tiyeni tidzingolima ngati zikuvuta atsikana 😂..osamauvutitsa moyo😉
13
6
59
@Tawonga70129690
Zwii♥️
3 months
Fasting in times of short days,long nights feels incredible... umangozindikira tsiku lavaya!!😉
2
8
53
@Tawonga70129690
Zwii♥️
8 months
This is me eating this after every meal I have had...waima pano ndani?kapena waimitsa nzake ndani pano😏
Tweet media one
12
1
52
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
"Chilango chili pansi pompano"..ever heard of this phrase??..I think it's a fact!
2
11
50
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
One thing I've learnt about life is,we plan but God decides,I made all plans that on 12 December being my birthday I would spoil myself like never before,not knowing that I will be burying my mother-in-law 😢..komabe mulungu salakwitsa!
12
0
50
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Sikuti ndi umbombo..koma with this economy, normalize buying something when going to your friends houses uninvited...osati "ndipezetu samoosa ndibwera Friday"..aah magaye 😂..ine nde ndamuuza ngati mufuna samoosa bring the mince..nyengo yavuta aliyense.
7
5
49
@Tawonga70129690
Zwii♥️
9 months
As the 6th year ends..the journey continues...anzanga a dreadlocks let's go to @EuphoriaMw ..wash and retouch zikutheka 😉
Tweet media one
7
4
48
@Tawonga70129690
Zwii♥️
4 months
Koma wangongole akati aname..iiih😆
7
9
49
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Hangover ya lero Mpaka kupanga nayo shiver🙄 Khangati Gin wake anali wa Moto😢
6
4
46
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Kuyesela kusaka mma handbag mose kuti mwina ndinaiwalamo fafandede,koma ayi ndithu😂 This December is not decembering me!!
5
3
46
@Tawonga70129690
Zwii♥️
7 months
Mpaka kutitchula mf chifukwa cha mulili wama caftan😂
@Same_Laz
WarmHeartWanderer🧸
7 months
Is she the same person??? 👀👀
8
4
22
4
5
43
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
If you want to talk to me,talk to me directly,,don't go through the corners😂😂komanso am too old to be someone's girlfriend 😂
@Untouched260
UNTOUCHED
1 year
😂 Imagine your girlfriend crying on Twitter ati Blesser kumpasa 30k yachepa kwambili
7
22
82
6
9
44
@Tawonga70129690
Zwii♥️
9 months
I must admit that I enjoy listening to Gospel songs, especially Hymns..zinazo can come after the Hymns ☺️...chi Presbyterian chinakhazikika!!
4
9
42
@Tawonga70129690
Zwii♥️
11 months
Being a Tonga,I don't know if the "I love you more than a cup of tea" would have worked for me...ineyo ndi Tea ndife pachibale,I wouldn't compromise it with anything except if it's Gin of course 🤭
9
4
43
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Ati today's weather is bae weather. Iwe shatapu..zaulesi basi😂go and hustle uko😂😂😂
2
7
43
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
All these stories of females having male besties I thought they were lies..apapa ndaona kuti anthudi Ali ndi ma best friends of opposite side 😂
6
9
38
@Tawonga70129690
Zwii♥️
8 months
Kambwiri sisters ija imakometsa nyimbo..🔥
3
4
39
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Dzukani tikapemphere.
Tweet media one
4
0
38
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
If you want to cheat,make sure you know how to cheat.✌️ Khangati tulo silinathe🥱
8
7
37
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
@Africanmonk11 Atsikana otere amandibhowa...
6
1
38
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Apart from calling 626 or going straight to the bank..how else can I communicate with National Bank??awawa ndiobowa
18
4
39
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 month
@Kamoza0104 Just imagining wearing that with this nyash😂eh eh..ma vendor okhawo...ma food warmer omwewa Ali well amwene.
12
2
37
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 months
Tell me about it...ana amasiku ano Alibe mantha iih..ngati ungokamenya khofi😂
@fluffy_bootie
Fluffy
2 months
Sindinadziwe kuti ndizafika pa stage yofusilidwa ndimwana wa zaka 19 at my old age. It's disturbing honestly 🤣🤣🤣
60
41
306
6
3
37
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
'kumva' ndi 'kumvetsetsa'..are two different things 🥱
1
9
36
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
Akazi akuluakulu amachuluka nzeru..ngati ineyo🤭
@_Mmasebotsana_
DIMAKATSO🌼
10 months
Why do most men like young women?
776
159
2K
7
4
35
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Every drunk person has something to say always when he/she has had enough...that was me yesterday telling two of my friends I was getting drunk with,,"aphwanga mkazangomva kuti mmandijeda nzakumenyani makofi simudzandifunanso"😂😂😂
7
2
35
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
Apparently I have been lying a lot about my age,so I met an old friend who happens to be my husband's nephew's friend,,the guy wauluratu zaka zathu nde mwanayu wapeza nkhanitu😂..ati aunt Kani ndinu mwana chonchi 😏..moti old friend yu ndimuchapa osati zibwana.
8
0
29
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Truth be told,,Matafale uja anali Makina!! Palibenso.
2
4
31
@Tawonga70129690
Zwii♥️
3 months
As I sat at the edge of the bed today in the morning,I found myself massaging my husband's feet unknowingly while telling him 'zolengeza'...to my surprise mnangomva.."ife nde zimenezo timangozionela mma video tu"..am like what?ati izozo za massage zo😂😂😂
9
4
32
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Tiyeni tisafooke tikunge inanso...kwacha kokha🔥
5
2
30
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 months
Times like this makes me wish if I had a friend with a one tan..😔😔ngati ndingoitayatu Irish potatoe yi ine.
4
4
30
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 months
I won't even remember that I made this tweet probably...but yohh.. I'm drunk..back to basics..Malawi Gin ndi m'bale😉
3
0
29
@Tawonga70129690
Zwii♥️
6 months
if i considered myself a lucky person,i would have submitted my idea without second thought....koma ineyo ndi mwai nde ndi kutalitali..best of luck y'all
@PempheroMphande
Pemphero W Mphande
6 months
In partnership with @RestaurantsKips , we embark on a 6 months journey to give away 18 million Kwacha in business capital to 18 people. 6 people per region. Join us!
Tweet media one
14
45
137
5
2
28
@Tawonga70129690
Zwii♥️
9 months
Komanso Gardener ku field akumakataniko?
10
1
29
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
We said goodbye to lilongwe this morning ♥️
Tweet media one
2
3
28
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
@winnieelphet Eti amwene...ine ndapanga manyazi on her behalf
5
3
27
@Tawonga70129690
Zwii♥️
7 months
Waking up to a dream of me having weed and a sip of Captain Morgan!!..satana wandilephera.
5
2
27
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Whenever I go to the market,there will always be a guy from nowhere hyping me unnecessarily,,umva 'mmakwana mama',,'muli bho sister'..at the end of all this hyping umva ka 2 Hanz bwanji😂😂..wtf..inenso ndiopempha magaye😂
3
0
28
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
@CEO_Ngozo Checking on him frequently...like are you okay?have you eaten?if you find time please eat☺️☺️since the way to a man's heart is food😂
5
1
26
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Zoduka mutu..I couldn't even finish reading..vya ziii
@Shadaya_Knight
𝑻𝒉𝒆 𝑺𝒂𝒍𝒕 𝑶𝒇 𝑻𝒉𝒆 𝑬𝒂𝒓𝒕𝒉
1 year
Lupita Nyongo in her 40s, walking away from her relationship because her man cheated is peak female delusion. Of cause, the sisterhood will support such stupidity with the rhetoric "you deserve better queen" as if there's any high value man out there waiting to pick up a 40 year
Tweet media one
5K
3K
13K
7
3
24
@Tawonga70129690
Zwii♥️
16 days
@AnzowFrank Nde ife okumwa titatufe?🤔
8
2
25
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
So I have taken my time and watched the movie 'Utopia'...now this movie got me thinking like,what if it's true??magaye inetu mnabaitsa katemera wa covid uja😂..nde ndufuna kubelekatu ine ohoo😂
4
2
25
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
This is how corrupt my mind is; Whenever I hear someone mentioning about Ndata farm that bingu left..mutu wanga umabalarika🤭 Also when one says something about "beans"..ndimaganiza udyo😂 Panopa sipabwino magaye.
9
0
24
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
@princestevens1 @zodiakonline I said it..kuti a Ras ndi munthu wa sharp🔥
1
1
25
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
DM kungodzadza ndi dzi ma link za Instagram chanichani zija..ayi zikomo 😂
5
1
25
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 years
Someone here wrote "no man can ever love a needy"...the more you show how desperate you are to men..the more they take advantage of your situation!!sis must heal already 😏
6
1
23
@Tawonga70129690
Zwii♥️
11 months
Oh oh😂
@GwambaOfficial
Gwamba 🇲🇼
9 years
@harawa_wendy Hahahahaha. Can I Fuck you and give you money?
79
127
148
9
2
24
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Wangongole wanga wangoona status yanga ku WhatsApp nthawi yomweyo ndakumbutsiratu ndalama yanga..zachamba ndimadana nazo😂
4
4
24
@Tawonga70129690
Zwii♥️
11 months
CDC akutanthauza chani?
7
1
22
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Tonse opanda ma connection tikudziwana!
6
3
23
@Tawonga70129690
Zwii♥️
10 months
People who pronounce Christmas as "Xmas"..ndatitu pronounce...are you okay?you mean "Christ" mkamwamo amakhala akulemera?? come on 😏
2
4
23
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Kodi ku Blantyre kulibe anthu aja amagula ngongole aja?
5
0
22
@Tawonga70129690
Zwii♥️
2 months
Same here😂..bufukeke odinda mu jean trouser..eheh
@KandyPure02
KP
2 months
I'm trying to do the opposite, damn
35
13
85
9
0
22
@Tawonga70129690
Zwii♥️
1 year
Ife kwathu kuli Azam TV😂
2
1
22
@Tawonga70129690
Zwii♥️
9 months
Komatu that "Mudyela" song nde sikuchoka mmutu mwangamu..😂it's strange because I despised that song masiku oyambilira..it's a nice song hey!
8
2
21