
Apula๐ฃ
@unrulyPulayive1
Followers
3K
Following
17K
Media
595
Statuses
18K
DAMN!
Africa
Joined September 2020
Pena business ikome Pena ikukumbutse kuti you have to apply for the jobs ๐ญ๐ญ๐๐๐
2
32
104
Ine ndichi sosa, iwe ndichinda? ๐ฉ๐
51
45
320
sometimes, I scratch my head and wonder if Lilongwe would have experienced this during any of DPPโs tenures.
58
23
242
1. Ine sindiliri pa mgwirizano ndi DPP -Kuvotera DPP ndikupha Malawi. Inuyo Mwayiwala kale nyasi zinali mu dziko muno nthawi ya DPP? Kusankhana mitundu, kupha anthu achi albino, katangale ndi umbava. -Mbava zambiri zomwe zikugwetsa ntchito za boma pano ndi za DPP. -Mukavotera DPP
10
8
33
Kuvota kuli apo kwinaku tiyeni tilimbikire guys. Mavuto ena boma silingathetse. Ulesi, nsanje, kaduka ndi zinzake. Tiyeni tikondane, tipatsane ma plan a business, tilembane ntchito, tipange ma gulu and get loans if possible. Chamba daily, mowa daily ndi zina zija sizitisunga.
55
313
667
Team News ๐ฉบ โ
Salima available โ Singo still out ๐ Chilipa eligible All set for Dedza Dynamos this Saturday ๐๐ฝ ๐ https://t.co/NZOsiD8hO3
#YesMaule #TNMSuperLeague #FCBNyasaBigBullets
nyasabigbullets.com
Chikumbutso Salima returns, but Yankho Singo and Chrispin Mapemba remain sidelined as Bullets face Dedza Dynamos in the TNM Super League
2
2
8
Silver Strikers return from the FIFA International break and dive straight into action as we play FC Shire in the Round of 16 of the 2025 FDH Cup. This is how the Central Bankers line up this afternoon:
1
4
12
Lawi has shared photos from his wedding with his wife. ๐๐ธ
13
79
670
Koma chamba guys Mpaka 32 songs one Album? Iyiyi ndiye tinvera mpaka 2099๐ฅ๐
20
34
224
Ngati mkuluyo ali uyuyu ine nde sindimamudziwa ndipo sinnamuonepo moyo wanga onse koma iye zimaoneka kuti amandidziwa bwino Kwabasi. Chidyereni mkazi chisanabereke chinzake, nzibambo wa nyima pakhosi uyu, mwana opusa kwambiri. May he suffer extremely from this embarrassment๐
32
39
192
Manchester United team yokhumudwitsa otsatira Ake.
3
15
53
FT: Songwe 1-3 Bullets ๐ดโช Babatunde โฝโฝ | Salima โฝ Three points secured in Karonga! ๐ช #SBUNBB #YesMaule #TNMSuperLeague
9
21
128
Ati IKK akati tabwelaso kenako chimadzana kuti lusoli ndi mphatso๐คฃ๐ญ
0
5
12
According to the FIFA schedule, the World Cup qualifier between the Flames and Liberia will take place under the floodlights at Bingu National Stadium, with kick-off set for 18:00 hrs on Monday, 8 September. #442Malawi
5
17
65