![__Mikateo Profile](https://pbs.twimg.com/profile_images/1801495355428622336/6-LX2MzD_x96.jpg)
__Mikateo
@__yahtallboyyyy
Followers
82
Following
169
Statuses
94
@itmustbewakisa @giftchauluka01 @malawi_truth I mean mwina adhawo akanangodya nkungokhala chete mwina moving on zikanakhalabe zomveka Koma mpaka challenging you and making jokes ah mayaz😂
1
0
2
@lucky96mw @Curtissapangano @Kauka_Af @malawi_truth Komanso it wasn't just tima relationship tafwakalalati. Bro wanted to marry that girl. Olo nane choipacho ntabwenzera straight
1
0
2
@KamphindaK @ElenimoC @giftchauluka01 @ChikondiChokho1 Weakness yo comes as a secondary effect Ka bwana. And of course masturbation is considered not harmful when done in moderation but I don't think someone would say "ineyo I masturbate once or twice a week " after time you'll get addicted and anything done in excess is harmful.
1
0
1
@djsurboowfer22 @ShadreckNthako @Dathreat99 Atsikana ndamene amaoangatu izi zomati tisonkhelane ma bwanji. Boys imangotengana kuti tiyeni pakuti tilibe nthawi yomawelengetsera kuti uyuyu wasonkha bwanji uyu wasonkha bwanji
2
0
2
@Brian5260881871 @Mfumu_Ya_Alomwe Well that's what boys do. Kaya food Kaya bawa timasonkha iliyonse yomwe ulinayo in fact pamapezekanso wina oti sanaike kalikonse komabe kufila chimodzimodzi
1
0
0
RT @SkayzTmg21: Munthu anatumiza parcel yama t-shirts a 84k thousand Monday town ya Lilongwe pa minbus imeneyi kut ikasiye ku area 25 sungw…
0
268
0
RT @Vardy_thee_goat: Macelba is dropping this Ep next week, please retweet for awareness 🔥 #ATS
0
7
0
RT @GauthXander: @malawi_truth Bottom line is.. magaye family issues are not for public consumption
0
6
0