![ESCOM Profile](https://pbs.twimg.com/profile_images/629127827804176385/3-2S9P51_x96.jpg)
ESCOM
@ESCOM_Malawi
Followers
26K
Following
104
Statuses
2K
We Procure, Transmit and Distribute electricity in Malawi. This is ESCOM's official twitter page. Power All Day Every Day!
Malawi
Joined August 2015
Imbani foni mwawulere pa nambala ya 847 (Airtel/Tnm) ndi kutidziwitsa za anthu amchitidwe wa chinyengo #SayNoToCorruption
#ESCOM #PowerAllDayEveryday
4
0
7
KUPELEKA MAVUTO OKHUDZA MAGETSI PA FONI KWAPHWEKA! imbani *2020#, sankhani 2, yankhani ndondomeko zotsatila kuti mupeleke vuto lomwe muli nalo mwatsatanetsane #ussdcode #escom360degreesdigitalplatforms
#ESCOM #PowerAllDayEveryday
1
0
2
Follow these safety precautions to avoid electricity-related in-door accidents #SafetyTips
#SafetyFirst
#ESCOM #PowerAllDayEveryday
0
0
1
Tsatirani njira izi kuti mukhale otetezeka ku ngozi zokhudzana ndi magetsi mnyumba mwanu #SafetyTips
#SafetyFirst
#ESCOM #PowerAllDayEveryday
0
0
1
BASOPU! Kukaniza a Escom kuti abwere pa nyumba panu kuzagwira ntchito ndimulandu ndipo muzalandila chilango chokakhala kundende ndi kulipiranso chindapusa chandalama pafupifupi 50 miliyoni #ElectricityAct
#SayNoToCorruption
#SayNoTOVandalism
#ESCOM #PowerAllDayEveyday
5
0
1
Tsatilani izi kuti mupewe ngozi zokhudzana ndi magetsi #SafetyFirst
#SafetyTips
#ESCOM #PowerAllDayEveryday
0
0
0
Dziwani za milandu ndi zilango zomwe zili mu lamulo la ntchito za magetsi #EletricityAct
#SayNoToCorruption
#SayNoToVandalism
#ESCOM #PowerAllDayEveryday
0
0
3
RETRIEVE YOUR MISSING OR LOST TOKENS FROM OUR 360 DEGREES DIGITAL PLATFORMS #EscomMobileApp
#EscomWebsite
#WhatsappChatbot
#EscomUSSDcode
1
0
5